Snow wa ku China
Ku mzinda wa Chengdu ku China, kuli malo amene amatchedwa 'Snow village'.
Kumakongola ndi snow ndipo ma tourist amapitako chifukwa cha mmene snow yo amakongolera.
Ulendo uno, anthu anadabwa kuti snow anali ochuluka chimodzimodzi mpaka padenga pa manyumba.
Zinthunzi pa social media page pawo zochititsa chidwi ndi snow koma kunali kukutentha osati kuzizira ndipo snow samasungunuka.
Atafufuza, apeza kuti anali snow wa fake. Anangoyika dzima cotton wool ndi thovu la soap (foam).
Atawafunsa, apepesa nkunena kuti samafuna kukhumudwitsa ma tourist.
Abweza ndalama za anthu omwe anapitako.
#Nkhani