Mayi odziwika ndi kukonda plastic surgery wamwalira
Mayi uyu, Jocelyne Wildenstein, anali otchuka kwambiri ndipo wamwalira ali ndi dzaka 84.
Jocelyne anali ochokera ku Switzerland ndipo anatchuka chifukwa amakonda kupanga plastic surgery nkhope yake kuti akongole moposa.
Jocelyne anapangitsa ma plastic surgery oposa 100.
Chifukwa choti samasiya kupangitsa plastic surgery, anapatsidwa nickname yokuti 'Catwoman' chifukwa cha shape ya maso ake chifukwa cha surgery.
Akuti wafera kutulo.