Mwana wa dzaka 8 wapulumuka masiku 5 mu nkhalango

Ku Zimbabwe, mwana uyu, wadzaka 8 anasowa ku game reserve kwa masiku 5.

Mwanayu, Tinotenda Pudu, anachoka kunyumba kwawo, kupita kosewera nkupezeka walowa mu Matusadonha Game Park, nkusochera.

Mu nkhalangoyi, muli mikango 40, Njovu ndi zinyama zambiri zowopsya.

Anthu ammudzi ndi ma game rangers anayamba kumusaka, osamupeza kwa masiku. Day 5, ndipamene ma game rangers anapeza ma footprint a mwana nkuyamba kulondola.

Nayenso atamva sound ya magalimoto, anathamangira konko.

Akuti Tinotenda amadya zipatso kuti achite survive.

Pano alikwawo safe.

Sidenote

Uyu akadzakula adzakhala Rambo kapena George of the jungle

#Nkhani

Previous
Previous

Mayi odziwika ndi kukonda plastic surgery wamwalira