2Baba Idibia wapeza mkazi wina
Oyimba wa ku Nigeria, 2baba Idibia analengeza kuti akumupanga divorce mkazi wake odziwika, Annie Idibia, pa 26 January.
Annie sanamvetse, kuzunguzika ndi heartbreak mpaka ali mchipatala (rehab). Amamukonda mamunayu modabwitsa.
Pangotha 2 weeks, 2baba watulutsa mkazi amene akufuna kukwatira, banja anafunsira kale, lawyer Natasha Osawaru.
Sakudikiranso kuti Annie akhale bwinobwino mentally. Akhala pa banja dzaka 20.
Natasha ali ndi dzaka 31, sanayambepo wakwatiwa, alibe mwana ndipo ndi ochoka ku banja lolemera kwambiri.
2Baba ali ndi ana 7, anawa anabadwa kwa azimayi atatu osiyana.
Sidenote
Never forget to love yourself
#Nkhani