Sister Claire - Ulendo okhala Saint

Mayi uyu, ndi Sister Claire Crocket, yemwe anali wa ku Ireland.

Sister Claire, anali actress poyamba koma atamva kuyitana kwa mzimu opera, anakakhala Nun mu mpingo wa Catholic.

Abale ake anali odabwa pa nthawiyo koma anawona kuti Sister Claire anali serious.

Kuyamba kutchuka kuti Sister Claire anali ndi m'dalitso ochiritsa anthu a mabvuto obereka (fertility issues) ndipo anthu angapo anachira.

Mu 2016, Sister Claire anapita ku Ecuador, kumene kunapangika chivomerezi ndipo Sister Claire anamwalira pa ngoziyi.

Sister Claire anali ndi dzaka 33.

Mpingo wakatolika wayamba mndondomeko oyikiza Sister Claire kuti akhale Saint.

Mwambo oyamba pa mndondomekowu, ndi beatification, umene utachitikire ku Spain.

Previous
Previous

Dingo wandidyera mwana

Next
Next

Uganda - Ayamba kupereka vaccine wa nthenda ya Ebola