Aphunzitsi amangidwa atabelekerana mwana ndi mwana wa dzaka 12

Ku USA, mayi uyu, Laura Coran, wa dzaka 34 wamangidwa.

Nkhani yake yatchuka kwambiri. Laura ndi mphunzitsi wa standard 5. Anayamba kucheza ndi makolo a student wake wa dzaka 12 (boy).

Ankamvana mpaka mwanayo amatha kukagona kunyumba kwa aphunzitsiwo.

Patadutsa nthawi, aphunzitsi (Laura) anabereka mwana. Makolo ake a student ataona mwanayo, anazunguzika mpaka anakalemba pa Facebook kuti 'mwana wa a teacher nkhope nde nde nde nde ndi mwana wanga'.

Ena ataona Facebook post, anakanena ku school mpaka panayambika kafukufuku.

Laura wamangidwa chifukwa papezeka umboni wakuti anapatsidwa mimba ndi student wake wa dzaka 12 mpaka kubereka mwana.

Sidenote

Laura amusandutsa chitsanzo kwa ena chifukwa uku ndi kugwililira

#Nkhani

Previous
Previous

Ndege yagwa ku South Sudan

Next
Next

Tizinyama totchedwa Koala tikutha chifukwa cha matenda opatsirana